-
1 Mafumu 10:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Pamasitepe 6 aja, panali zifaniziro 12 za mikango itaimirira. Kumapeto kwa sitepe iliyonse kunali mkango umodzi. Panalibenso ufumu womwe unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.
-