1 Mafumu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ zomwe zinkayenda panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:22 Nsanja ya Olonda,11/1/2008, tsa. 27
22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ zomwe zinkayenda panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko.