1 Mafumu 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Anthuwo ankabweretsa mphatso monga zinthu zasiliva, zinthu zagolide, zovala, zida zankhondo, mafuta a basamu, mahatchi komanso nyulu* ndipo zimenezi zinkachitika chaka chilichonse.
25 Anthuwo ankabweretsa mphatso monga zinthu zasiliva, zinthu zagolide, zovala, zida zankhondo, mafuta a basamu, mahatchi komanso nyulu* ndipo zimenezi zinkachitika chaka chilichonse.