1 Mafumu 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Solomo anasonkhanitsa magaleta ndi mahatchi,* moti anali ndi magaleta 1,400 komanso mahatchi* 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+
26 Solomo anasonkhanitsa magaleta ndi mahatchi,* moti anali ndi magaleta 1,400 komanso mahatchi* 12,000.+ Zonsezi ankazisunga mʼmizinda yosungiramo magaleta ndiponso pafupi ndi mfumuyo ku Yerusalemu.+