1 Mafumu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Galeta lililonse lochokera ku Iguputo mtengo wake unali ndalama zasiliva 600 pomwe mtengo wa hatchi unali ndalama zasiliva 150. Ndipo iwo ankagulitsa zinthuzi kwa mafumu onse a Ahiti+ ndi mafumu a ku Siriya. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:29 Galamukani!,11/2010, tsa. 16
29 Galeta lililonse lochokera ku Iguputo mtengo wake unali ndalama zasiliva 600 pomwe mtengo wa hatchi unali ndalama zasiliva 150. Ndipo iwo ankagulitsa zinthuzi kwa mafumu onse a Ahiti+ ndi mafumu a ku Siriya.