1 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu Solomo inakondanso akazi ena ambiri a mitundu ina+ kuwonjezera pa mwana wamkazi wa Farao.+ Inakonda akazi a Chimowabu,+ a Chiamoni,+ a Chiedomu, a Chisidoni+ ndi a Chihiti.+
11 Mfumu Solomo inakondanso akazi ena ambiri a mitundu ina+ kuwonjezera pa mwana wamkazi wa Farao.+ Inakonda akazi a Chimowabu,+ a Chiamoni,+ a Chiedomu, a Chisidoni+ ndi a Chihiti.+