1 Mafumu 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Akaziwa anali ochokera mʼmitundu imene Yehova anauza Aisiraeli kuti: “Musamakwatirane nawo komanso musamacheze nawo, chifukwa adzapotoza mitima yanu kuti muzitsatira milungu yawo.”+ Koma Solomo ankakonda anthu amenewa ndipo sanafune kuwasiya.
2 Akaziwa anali ochokera mʼmitundu imene Yehova anauza Aisiraeli kuti: “Musamakwatirane nawo komanso musamacheze nawo, chifukwa adzapotoza mitima yanu kuti muzitsatira milungu yawo.”+ Koma Solomo ankakonda anthu amenewa ndipo sanafune kuwasiya.