1 Mafumu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anali ndi akazi olemekezeka 700 komanso akazi ena apambali 300 ndipo patapita nthawi, akaziwo anapotoza mtima wa Solomo.*
3 Iye anali ndi akazi olemekezeka 700 komanso akazi ena apambali 300 ndipo patapita nthawi, akaziwo anapotoza mtima wa Solomo.*