1 Mafumu 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova anabweretsa munthu woti azilimbana ndi Solomo.+ Munthuyo anali Hadadi wa ku Edomu ndipo anali wa mʼbanja lachifumu ku Edomuko.+
14 Kenako Yehova anabweretsa munthu woti azilimbana ndi Solomo.+ Munthuyo anali Hadadi wa ku Edomu ndipo anali wa mʼbanja lachifumu ku Edomuko.+