1 Mafumu 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawi imene Davide anagonjetsa Edomu,+ Yowabu, mkulu wa asilikali, anapita kukakwirira anthu amene anaphedwa. Kumeneko anayambanso kupha mwamuna aliyense wa ku Edomu.
15 Pa nthawi imene Davide anagonjetsa Edomu,+ Yowabu, mkulu wa asilikali, anapita kukakwirira anthu amene anaphedwa. Kumeneko anayambanso kupha mwamuna aliyense wa ku Edomu.