1 Mafumu 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu anabweretsa munthu winanso woti azilimbana ndi Solomo.+ Munthuyo anali Rezoni mwana wa Eliyada, yemwe anathawa kwa mbuye wake Hadadezeri,+ mfumu ya Zoba.
23 Mulungu anabweretsa munthu winanso woti azilimbana ndi Solomo.+ Munthuyo anali Rezoni mwana wa Eliyada, yemwe anathawa kwa mbuye wake Hadadezeri,+ mfumu ya Zoba.