1 Mafumu 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide atagonjetsa* anthu a ku Zoba, Rezoni anasonkhanitsa anthu ndipo anakhala mtsogoleri wa gulu la achifwamba.+ Choncho iye ndi gulu lakelo anapita kukakhala ku Damasiko+ nʼkuyamba kulamulira kumeneko.
24 Davide atagonjetsa* anthu a ku Zoba, Rezoni anasonkhanitsa anthu ndipo anakhala mtsogoleri wa gulu la achifwamba.+ Choncho iye ndi gulu lakelo anapita kukakhala ku Damasiko+ nʼkuyamba kulamulira kumeneko.