1 Mafumu 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anaukira mfumu chifukwa chakuti: Solomo anamanga Chimulu cha Dothi*+ ndiponso anatseka mpata umene unali pampanda wa Mzinda wa bambo ake Davide.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2152
27 Iye anaukira mfumu chifukwa chakuti: Solomo anamanga Chimulu cha Dothi*+ ndiponso anatseka mpata umene unali pampanda wa Mzinda wa bambo ake Davide.+