1 Mafumu 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yerobowamu anali munthu waluso. Ndiyeno Solomo ataona kuti mnyamatayo ndi wolimbikira ntchito, anamʼpatsa udindo woyangʼanira+ anthu ogwira ntchito yokakamiza kunyumba ya Yosefe.
28 Yerobowamu anali munthu waluso. Ndiyeno Solomo ataona kuti mnyamatayo ndi wolimbikira ntchito, anamʼpatsa udindo woyangʼanira+ anthu ogwira ntchito yokakamiza kunyumba ya Yosefe.