1 Mafumu 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pa nthawiyo, Yerobowamu anatuluka mu Yerusalemu ndipo Ahiya+ wa ku Silo, yemwe anali mneneri, anamʼpeza panjira. Ahiya anali atavala chovala chatsopano ndipo awiriwo anali okhaokha kumeneko.
29 Pa nthawiyo, Yerobowamu anatuluka mu Yerusalemu ndipo Ahiya+ wa ku Silo, yemwe anali mneneri, anamʼpeza panjira. Ahiya anali atavala chovala chatsopano ndipo awiriwo anali okhaokha kumeneko.