-
1 Mafumu 11:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ndichita zimenezi chifukwa iwo andisiya+ nʼkuyamba kugwadira Asitoreti mulungu wamkazi wa Asidoni, Kemosi mulungu wa Amowabu ndi Milikomu mulungu wa Aamoni. Iwo sanayende mʼnjira zanga, sanachite zoyenera pamaso panga ndipo sanatsatire malamulo anga ndi ziweruzo zanga ngati mmene anachitira Davide bambo a Solomo.
-