1 Mafumu 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mwana wake ndidzamʼpatsa fuko limodzi kuti mtumiki wanga Davide apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mumzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha kuti ukhale ndi dzina langa.
36 Mwana wake ndidzamʼpatsa fuko limodzi kuti mtumiki wanga Davide apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mumzinda wa Yerusalemu+ umene ndausankha kuti ukhale ndi dzina langa.