1 Mafumu 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Solomo ankafuna kupha Yerobowamu koma Yerobowamu anathawira ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo.+ Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:40 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, tsa. 30
40 Solomo ankafuna kupha Yerobowamu koma Yerobowamu anathawira ku Iguputo kwa Sisaki,+ mfumu ya Iguputo.+ Anakhala ku Iguputoko mpaka Solomo atamwalira.