1 Mafumu 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kenako Solomo anamwalira* ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide bambo ake. Ndiyeno mwana wake Rehobowamu,+ anakhala mfumu mʼmalo mwake. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:43 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, tsa. 31
43 Kenako Solomo anamwalira* ndipo anaikidwa mʼmanda mu Mzinda wa Davide bambo ake. Ndiyeno mwana wake Rehobowamu,+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.