1 Mafumu 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Rehobowamu anapita ku Sekemu+ chifukwa Aisiraeli onse anapita kumeneko kuti akamuveke ufumu.+