1 Mafumu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu anafunsa nzeru kwa anthu achikulire* amene ankatumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Anawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”
6 Ndiyeno Mfumu Rehobowamu anafunsa nzeru kwa anthu achikulire* amene ankatumikira bambo ake Solomo pamene anali moyo. Anawafunsa kuti: “Kodi mukuganiza kuti anthuwa ndiwayankhe bwanji?”