-
1 Mafumu 12:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Inayankha anthuwo motsatira malangizo a achinyamata aja. Inati: “Bambo anga anakusenzetsani goli lolemera koma ineyo ndiwonjezera goli lanulo. Bambo anga ankakukwapulani ndi zikwapu koma ineyo ndizikukwapulani ndi zikoti zaminga.”
-