1 Mafumu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho mfumu sinamvere anthuwo. Yehova ndi amene anachititsa kuti zinthu zikhale chonchi,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula kwa Yerobowamu mwana wa Nebati kudzera mwa Ahiya+ wa ku Silo.
15 Choncho mfumu sinamvere anthuwo. Yehova ndi amene anachititsa kuti zinthu zikhale chonchi,+ kuti akwaniritse mawu amene Yehovayo analankhula kwa Yerobowamu mwana wa Nebati kudzera mwa Ahiya+ wa ku Silo.