-
1 Mafumu 12:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Aisiraeli onse ataona kuti mfumuyo yakana kuwamvera, anayankha kuti: “Ife Davide tilibe naye ntchito ndipo sitingapatsidwe cholowa kuchokera kwa mwana wa Jese. Aisiraeli inu, aliyense apite kwa milungu yake! Tsopano iwe Davide, uziyangʼanira nyumba yako yokha.” Aisiraeliwo atatero, aliyense anabwerera kunyumba* kwawo.+
-