1 Mafumu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Adoramu+ amene ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma Aisiraeli onse anamugenda ndi miyala nʼkumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta lake nʼkuthawira ku Yerusalemu.+
18 Kenako Mfumu Rehobowamu inatumiza Adoramu+ amene ankayangʼanira anthu ogwira ntchito yokakamiza, koma Aisiraeli onse anamugenda ndi miyala nʼkumupha. Komabe, Mfumu Rehobowamu inatha kukwera galeta lake nʼkuthawira ku Yerusalemu.+