1 Mafumu 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatulapo fuko la Yuda.+
20 Aisiraeli onse atangomva kuti Yerobowamu wabwera, anatumiza uthenga womuitanira kumene anasonkhana, ndipo anamuika kukhala mfumu ya Aisiraeli onse.+ Palibenso amene ankatsatira nyumba ya Davide kupatulapo fuko la Yuda.+