1 Mafumu 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova wanena kuti: “Musapite kukamenyana ndi abale anu, Aisiraeli. Aliyense abwerere kunyumba chifukwa ine ndi amene ndachititsa zimenezi.”’”+ Choncho anthuwo anamvera mawu a Yehova nʼkubwerera kwawo ngati mmene Yehova ananenera. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2018, tsa. 14
24 ‘Yehova wanena kuti: “Musapite kukamenyana ndi abale anu, Aisiraeli. Aliyense abwerere kunyumba chifukwa ine ndi amene ndachititsa zimenezi.”’”+ Choncho anthuwo anamvera mawu a Yehova nʼkubwerera kwawo ngati mmene Yehova ananenera.