1 Mafumu 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthuwa akapitiriza kupita kukapereka nsembe kunyumba ya Yehova ku Yerusalemu,+ mtima wawo udzabwerera kwa mbuye wawo Rehobowamu mfumu ya Yuda. Akatero adzandipha nʼkubwerera kwa Rehobowamu mfumu ya Yuda.”
27 Anthuwa akapitiriza kupita kukapereka nsembe kunyumba ya Yehova ku Yerusalemu,+ mtima wawo udzabwerera kwa mbuye wawo Rehobowamu mfumu ya Yuda. Akatero adzandipha nʼkubwerera kwa Rehobowamu mfumu ya Yuda.”