-
1 Mafumu 12:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Yerobowamu anapereka nsembe pa tsiku la 15 la mwezi wa 8 womwe anausankha yekha. Anapereka nsembezo paguwa limene anamanga ku Beteli. Iye anayambitsa chikondwerero choti Aisiraeli azichita ndipo anakwera paguwa kukapereka nsembe zautsi komanso nsembe zina.
-