1 Mafumu 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Panali munthu wa Mulungu+ amene anatumidwa ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti apereke nsembe yautsi.
13 Panali munthu wa Mulungu+ amene anatumidwa ndi Yehova kuchokera ku Yuda kupita ku Beteli. Kumeneko iye anapeza Yerobowamu ataimirira pambali pa guwa lansembe+ kuti apereke nsembe yautsi.