-
1 Mafumu 13:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Mneneri wokalambayo atamva zimenezi anati: “Inenso ndine mneneri ngati iweyo. Mngelo wandiuza mawu ochokera kwa Yehova akuti, ‘Kamʼbweze upite naye kunyumba kwako kuti akadye chakudya ndi kumwa madzi.’” (Anamunamiza.)
-