-
1 Mafumu 13:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndiyeno mneneriyo ananyamula mtembo wa munthu wa Mulungu woonayo nʼkuukweza pabulu ndipo anabwerera nawo mumzinda wa mneneri wokalambayo kuti akamulire ndi kumuika mʼmanda.
-