1 Mafumu 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atamuika mʼmanda, mneneri wokalambayo anauza ana ake kuti: “Ndikadzamwalira mudzandiike mʼmanda amene taika munthu wa Mulungu woonayu. Mudzaike mafupa anga pambali pa mafupa ake.+
31 Atamuika mʼmanda, mneneri wokalambayo anauza ana ake kuti: “Ndikadzamwalira mudzandiike mʼmanda amene taika munthu wa Mulungu woonayu. Mudzaike mafupa anga pambali pa mafupa ake.+