1 Mafumu 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mawu a Yehova amene munthu wa Mulunguyu ananena otemberera guwa lansembe limene lili ku Beteli ndiponso akachisi onse amʼmalo okwezeka+ amene ali mʼmizinda ya ku Samariya, adzakwaniritsidwa ndithu.”+
32 Mawu a Yehova amene munthu wa Mulunguyu ananena otemberera guwa lansembe limene lili ku Beteli ndiponso akachisi onse amʼmalo okwezeka+ amene ali mʼmizinda ya ku Samariya, adzakwaniritsidwa ndithu.”+