1 Mafumu 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ngakhale kuti zimenezi zinachitika, Yerobowamu sanasiye kuchita zoipa. Iye anapitiriza kuika anthu wamba kuti akhale ansembe a malo okwezeka.+ Aliyense wofuna unsembewo, iye ankamʼpatsa ponena kuti: “Uyu akhale wansembe wa malo okwezeka.”+
33 Ngakhale kuti zimenezi zinachitika, Yerobowamu sanasiye kuchita zoipa. Iye anapitiriza kuika anthu wamba kuti akhale ansembe a malo okwezeka.+ Aliyense wofuna unsembewo, iye ankamʼpatsa ponena kuti: “Uyu akhale wansembe wa malo okwezeka.”+