1 Mafumu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Yerobowamu anauza mkazi wake kuti: “Nyamuka upite ku Silo ndipo udzisinthe kuti anthu asadziwe kuti ndiwe mkazi wa Yerobowamu. Mneneri Ahiya ali kumeneko. Iye ndi amene anandiuza kuti ndidzakhala mfumu ya anthuwa.+
2 Choncho Yerobowamu anauza mkazi wake kuti: “Nyamuka upite ku Silo ndipo udzisinthe kuti anthu asadziwe kuti ndiwe mkazi wa Yerobowamu. Mneneri Ahiya ali kumeneko. Iye ndi amene anandiuza kuti ndidzakhala mfumu ya anthuwa.+