1 Mafumu 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma Yehova anali atauza Ahiya kuti: “Kukubwera mkazi wa Yerobowamu kudzakufunsa za mwana wake chifukwa mwanayo akudwala. Ndikuuza zoti umuuze.* Akafika adzisintha kuti asadziwike.”
5 Koma Yehova anali atauza Ahiya kuti: “Kukubwera mkazi wa Yerobowamu kudzakufunsa za mwana wake chifukwa mwanayo akudwala. Ndikuuza zoti umuuze.* Akafika adzisintha kuti asadziwike.”