-
1 Mafumu 14:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Munthu wa mʼbanja la Yerobowamu wofera mumzinda, agalu adzamudya ndipo wofera kutchire, mbalame zidzamudya chifukwa Yehova wanena zimenezi.”’
-