-
1 Mafumu 14:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Aisiraeli onse akamulira nʼkumuika mʼmanda ndipo mʼbanja lonse la Yerobowamu, uyu yekha ndi amene adzaikidwe mʼmanda chifukwa mʼnyumba yonse ya Yerobowamu, Yehova Mulungu wa Isiraeli wapeza chinachake chabwino mwa yekhayu.
-