1 Mafumu 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzaika yekha mfumu ina yolamulira Isiraeli, yomwe idzafafanize nyumba ya Yerobowamu+ kuyambira tsiku limenelo, ndipo akhoza kuchitanso zimenezi pompano. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:14 Yesaya 1, ptsa. 133-134
14 Yehova adzaika yekha mfumu ina yolamulira Isiraeli, yomwe idzafafanize nyumba ya Yerobowamu+ kuyambira tsiku limenelo, ndipo akhoza kuchitanso zimenezi pompano.