1 Mafumu 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, mmene anamenyera nkhondo+ ndiponso ulamuliro wake, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.
19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, mmene anamenyera nkhondo+ ndiponso ulamuliro wake, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.