1 Mafumu 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yerobowamu analamulira zaka 22, kenako mofanana ndi makolo ake anamwalira.+ Ndiyeno mwana wake, dzina lake Nadabu, anayamba kulamulira mʼmalo mwake.+
20 Yerobowamu analamulira zaka 22, kenako mofanana ndi makolo ake anamwalira.+ Ndiyeno mwana wake, dzina lake Nadabu, anayamba kulamulira mʼmalo mwake.+