1 Mafumu 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nawonso anapitiriza kumanga malo okwezeka, zipilala zopatulika ndi mizati yopatulika*+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wamasamba obiriwira.+
23 Nawonso anapitiriza kumanga malo okwezeka, zipilala zopatulika ndi mizati yopatulika*+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wamasamba obiriwira.+