1 Mafumu 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye anatenga chuma chamʼnyumba ya Yehova ndi chuma chamʼnyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zonse zagolide zimene Solomo anapanga.+
26 Iye anatenga chuma chamʼnyumba ya Yehova ndi chuma chamʼnyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zonse zagolide zimene Solomo anapanga.+