1 Mafumu 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Mfumu Rehobowamu anapanga zishango zakopa* mʼmalomwake ndipo anazipereka kwa akulu a asilikali* olondera pakhomo la nyumba ya mfumu kuti aziziyangʼanira.
27 Choncho Mfumu Rehobowamu anapanga zishango zakopa* mʼmalomwake ndipo anazipereka kwa akulu a asilikali* olondera pakhomo la nyumba ya mfumu kuti aziziyangʼanira.