1 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:29 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 32
29 Nkhani zina zokhudza Rehobowamu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda.+