1 Mafumu 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Rehobowamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Mayi ake anali Naama ndipo anali a Chiamoni.+ Kenako Abiyamu*+ mwana wa Rehobowamu anayamba kulamulira mʼmalo mwake.
31 Kenako Rehobowamu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Mayi ake anali Naama ndipo anali a Chiamoni.+ Kenako Abiyamu*+ mwana wa Rehobowamu anayamba kulamulira mʼmalo mwake.