1 Mafumu 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, chifukwa cha kukhulupirika kwa Davide,+ Yehova Mulungu wake anamʼpatsa nyale mu Yerusalemu+ pokweza mwana wake pambuyo pake ndiponso pochititsa kuti Yerusalemu akhalepobe.
4 Komabe, chifukwa cha kukhulupirika kwa Davide,+ Yehova Mulungu wake anamʼpatsa nyale mu Yerusalemu+ pokweza mwana wake pambuyo pake ndiponso pochititsa kuti Yerusalemu akhalepobe.