1 Mafumu 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Masiku onse a Rehobowamu, pankachitika nkhondo pakati pa iyeyo ndi Yerobowamu.+