1 Mafumu 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Asa anachita zabwino pamaso pa Yehova+ ngati mmene anachitira Davide kholo lake.